Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Noma more fire
Nbb vs ntopwa
Defending Champions of FISD Cup Challenge, BE FORWARD Wanderers, are through to quarter finals stage of the competition after beating Masters Security 3 nil. Zulu, Botoman and Kaziputa netted the goals.
Khuda Muyaba now leads in the TNM Super League after netting a goal against Mzuni today.
Khuda now has 15 goals followed by Wanderers striker, Babatunde Adebayo with 14 goals.
Wosewera mmbali mu timu ya Blue Eagles, Vitumbuko Kumwenda, sapezeka pa masewero a timuyi ndi MAFCO mu FISD kaamba kovulala.
Mphunzitsi wa timuyi, Deklerk Msakakuona, watsimikiza za nkhaniyi.
Anthu ena okonda masewero mdziko muno ayankhulapo za chibaluwa chomwe chikuyenda masamba a mchezo choonetsa zomwe a Nyamilandu achita.
Anthu-wa ayamikira mtsogoleri-yu koma ati asapikisane nawo.
Bungwe lolimbikitsa maufulu la HRDC lati likhale likuuza aMalawi zomwe lipeze pomwe lati likufufuza kuphwanyilidwa kwa maufulu a anthu ku bungwe la FAM patsogolo pa chisankho cha bungwe-li.
Atalengeza kuti sadzatumikiraso timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Lucky Malata, waitanidwa kuti atenge nawo mbali pa zokonzekera za Flames kuyambira Lolemba.
Khuda Muyaba waitanidwa ndi mphunzitsi wa Flames kuti akachite nawo zokonzekera za timuyi.
Izi zikutsaira kudutsa kwa nthawi osewera-yu asakuitanidwa kaamba kolephera kusunga mwambo.
Mtsogoleri wa osewera wa timu ya MAFCO, Paul Ndlovu, wati ali ndi chikhulupiliro kuti abwelera mu ligi ya TNM potengera momwe akuchitira.
Osewera a timu ya Wanderers Lachinayi alandira ndalama zawo za masewero awiri.
Izi zikudza pomwe timuyi ili ndi masewero mu mpikisano wa FISD Loweluka likudza-li.
Charles Petrol will miss Bullets game against Ntopwa over the weekend due to injury.
Petrol has been added to the list of players who are injured at the club like Msowoya, Zonda, Mwakifuna Sailesi.
James Mwenda one of the Presidential aspirant is set to release his manifesto on Monday.
The manifesto is tittled 4 pillars.
Mwenda is the Vice President of FAM and he is challenging his boss.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Flames ikuyembekezeka kuyamba zokonzekera zake Lolemba likudza-li.
Aphunzitsi a timu-yi atulutsa ndandanda wa osewera omwe ayambe zokonzekera-zi Lachisanu.
Atakhala masiku awiri asakuchita zokonzekera osewera a timu ya Blue Eagles lero anachita zokonzekera zawo.
Izi ndi malingana ndi zomwe osewera awuza Owinna.
Flames have maintained position 124 in the World on latest FIFA rankings released today.
#Malawi U-20 Coaching Panel
Head Coach: Peter Mponda
Assistant Coach: Audral Makonyora
Team Manager: Aubrey Nankhuni
Goalkeeper's Trainer: Sibusiso Padambo
Peter Mponda has been appointed as Malawi National Football Team U-20 coach.
This is according to some FAM officials.
Mponda will be deputised by Audral Makonyora.
Masters Security has recruited Audral Makonyora as the new coach for the team.
General Secretary for the club, Christopher Njeura, has confirmed the development.
One of the FAM Presidential aspirant, Balawala Vingula, says once voted into power he will end JUJU beliefs in football fraternity.
This is according to the manifesto he has released.
ine ndimasapota nyasa bb
Blue Eagles players have started boycotting training due to unpaid bonuses.
Owinna understands that the players have not received their allowances for 12 games.
Bungwe la Sulom kuyambira pa 24 October lati osewera akunja amene samakhala zikalata zovomelezeka zokhalira mdziko muno ndi kugwira ntchito, work permit m'chingerezi samaloleswa kusewera mpira.
Pomwe patsala mwezi umodzi kuti timu ya mpira wa miyendo ya U-20 ikatenge nawo mu mpikisano wa COSAFA, timuyi idakalibe aphunzitsi.
Izi zili chomwe-chi kaamba koti aphunzitsi akale a timuyi anasiya.
Kwathu kuno ku Malawi-tu palibe vuto olo itakhala derby, masewero achitanyu, osewera osalandira mphoto ija timati Man of The Match, palibe amayankhula zimakhala zili khenge.
#Mpira pa Nyasaland.
Blue Eagles yalembera kalata Sulom podandaula kuti Mzuni inagwilitsa ntchito osewera ena omwe anali osaloledwa kusewera masewero awo.
Wapampando wa timuyi, Alexander Ngwala, watsimikizira izi Owinna.
Civil Sporting Coach, Eliah Kananji, is optimistic of finishing in top 4 of TNM Super League.
Kanjani made the sentiments following 2 consecutive defeats in Blantyre.
FAM President, Walter Nyamilandu, says Malawi is ready to host COSAFA Senior Football Tournament come 2021.
Nyamilandu says Malawi has the infrastructure to host the competition.
Matimu omwe anafika mu ndime ya matimu 16 mu mpikisano wa FISD ayamba ntchito yozipera malo amu quarter finals kumathero a sabata ino.
Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe FAM yatulutsa.
Big Bullets