Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Central Region Football Association (CRFA) Loweruka masana lapereka mphoto kwa matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu season ya 2018.
Malawi Under 23 will today start residential camping.
The Junior team is preparing for the 2019 U23 second round qualifier against Zambia in March.
BE FORWARD Wanderers is inviting all interested players who want to join the club to participate in trials which the team is expected to conduct from 4 February, 9:00 AM at Kamuzu Stadium.
BE FORWARD Wanderers Left back, Stanley Sanudi has dismissed reports that he is leaving Wanderers to join one of country's local team.
Sanudi says he has a contract with Wanderers.
Katswiri otchinga pa golo pa Masters Security ali m'chitokosi cha apolisi ku Area 2, Lilongwe atadyera timu ina ndalama.
Wadyera timu yanji? Be realistic
Timu ya Airborne Rangers yakhala akatswiri a chikho cha Inter Unit Sports Festival atagonjetsa Kamuzu Barracks ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi.
Central Region Football Association (CRFA) lero ipereka mphoto kwa matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu season ya 2018. Mwambowu ukachitikira ku Mbolembole Motel kuyambira nthawi ya half 4.
TN Stars has new executive members to lead the club in 2019 season. Current Chairman of the team is Mr Eliyasi (Kupata) Yasin.
Zacharia Nyirenda has resigned as General Secretary for Masters Security.
Nyirenda has confirmed the development saying he wants to contest for the post of Vice General Secretary of Sulom.
3 February 2019 Linthipe 3 stars VS Masters Security Time: 2:30 Venue:Nthulu Primary Schoool Ground
Renovation works at Chiwembe Stadium in Blantyre expected to be concluded before the kick-off of 2019 season.
Meanwhile the stadium is taking its shape.
Flames will play against Eswatini in first round of the 2020 CAF Total African Nations Champions Qualifiers, Ethopia 2020 Southern Zonal Qualifiers.
Precious Sambani, Peter Banda and Pilirani Mapira are yet to report for Flames training despite their call up.
The three were supposed to be in camp (Blantyre) last week.
Matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu mpikisano wa Fisd akuyembekezeka kulandira ndalama zawo posachedwapa.
Mmodzi mwa akuluakulu ku kampani ya Fisd, Wezi Chiumia watsimikiza za nkhani-yi.
One of the talented Malawi's forward, Robin Ngalande has signed an 18 months contract with Zira FC in Europe.
Osewera kutsogolo kwa Nyasa Big Bullets, Mussa Manyenje wati ndi khumbo lake kuti atenge mphoto ya katswiri omwetsa zigoli mu mpikisano wa TNM Super League.
koma zitheka
Ophunzira okhuzidwa pa sukulu ya ukachenjede ya Mzuni alembera kalata akuluakulu a sukulu-yi kuti asinthe ganizo lawo losiya kuthandiza osewera omwe si apa sukulu-pa.
Chitetezo Mbaula Southern Region Football Association in conjunction with United Purpose will hold the 2018 prize presentation on 4 February at Serendib Suites in Namiwawa, Blantyre.
Akuluakulu oyendetsa ligi ya kumpoto ya SIMSO sanabwerebe poyera ndi kufotokoza tsiku lomwe apereke mphoto ku matimu komanso osewera omwe anachita bwino mu mpikisano-wu.
Matimu a Airborne Rangers, Cobbe Barracks, MAFCO, Support Battalion, Changalume Barracks, Chilumba barracks, MDF Marine ndi Zomba Airwing akuyembekezeka kusewera nawo mu mpikisano wa Inter Unit Sports.
Wawa
Blue Eagles will start preparations of 2019 season today Tuesday.
Media Officer of the team, Steve Kumalonje has confirmed this in an interview with Owinna.
Chitipa United will commence preparations of 2019 TNM Super League today Tuesday.
Team Manager of the club, Watson Kabaghe has confirmed the development.
Timu ya Airborne Rangers yayamba kuchita zokonzekera za season ya 2019.Malipoti omwe yapeza Owinna timu-yi yasaina osewera mbali kuchokera ku Mangochi, Michael yemwe akuchita naye zokonzekera limodzi.
Former Parliamentarian Speaker and DPP aspiring member of parliament for Nkhotakota North constituency, Henry Chimunthu Banda has donated 500 hundred thousand Kwacha to Dwangwa United.
Peter Cholopi, BE FORWARD Wanderers player has dismissed reports that he wants to join another club locally. Cholopi said he has a contract with Wanderers.