Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Chicken Inn are the champions of Energem International Bonanza after winning 2 nil against UD Songo.
The team has won all the three games they have played in the competition.
Matimu a Bullets ndi Wanderers akumana masana-wa mu mpikisano wa Energem International Bonanza.
Awa ndi masewero omaliza pakati pa matimu awiri-wa.
Masewero-wa achitikira pa bwalo la Kamuzu.
Timu ya Chicken Inn ili ndi mwayi otenga ukatswiri wa Energem International Bonanza ngati itapambana kapena kufanana mphamvu ndi UD Songo.