Tiyamikire otsatira timu ya Wanderers pomwe kangapo konse athandiza osewera a timu yawo ndi zinthu zosiyanasiyana.
Kangapo konse otsatira timuyi apereka ndalama, zokudya komanso madzi kwa osewera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores