Akuluakulu oyendetsa ligi ya SIMSO mawa akonza mkumano ndi matimu omwe amasewera mu ligi-yi.
Masiya Nyasulu ndiye wanena izi poyankhula ndi Owinna.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores