Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
www.Mamuna Ndakhey .com
Fixture
FDH BANK CUP QUARTER FINAL DRAW
Changalume Barracks vs Extreme Nyasa Big Bullets Reserve vs Blue Eagles Mighty Wanderers vs Kamuzu Barracks Chitipa United vs Nyasa Big Bullets
Draw
Ndalama zokwana K19,500,000 ndizomwe zinapezeka pa masewero a Dedza Dynamos Salima Sugar ndi Mighty Mukuru Wanderers mumpikisano wa FDH Bank.
Aka ndikoyamba kuti pa bwalo la Dedza papezeke ndalama zochuluka chonchi kuchokera m'zipata.
Timu ina iliyonse inalandira ndalama zokwana K4,217,622. Timu ya Wanderers inapambana masewero-wa 0-3.
Katswiri wosewera kutsogolo kwa timu ya Moyale Barracks Lloyd Njaliwa akutsogola pa ndandanda wa omwetsa zigoli m'mpikisano wa FDH Bank ndi zigoli zitatu.
Njaliwa akutsatilidwa ndi Davie Major, Gastin Simkonda, Lanjesi Nkhoma komans Zeliat Nkhoma omwe amwetsa zigoli ziwiri aliyense.