Ndalama zokwana K19,500,000 ndizomwe zinapezeka pa masewero a Dedza Dynamos Salima Sugar ndi Mighty Mukuru Wanderers mumpikisano wa FDH Bank.
Aka ndikoyamba kuti pa bwalo la Dedza papezeke ndalama zochuluka chonchi kuchokera m'zipata.
Timu ina iliyonse inalandira ndalama zokwana K4,217,622. Timu ya Wanderers inapambana masewero-wa 0-3.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores