Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Ecobank Charity Shield Draw.
Nyasa Big Bullets vs BE FORWARD Wanderers
Silver Strikers vs Blue Eagles.
EcoBank Charity Shield will be played on 04th and 05th April.
This has been announced at a joint press briefing of FAM and EcoBank in Blantyre. EcoBank will sponsor 2020 Charity Shield with 18 million.
Football Association of Malawi (FAM ) yet to comment on reports circulating on social media of EcoBank Charity Shield postponment to April this year.
FAM will today hold a presser on the matter.
Yemwe anali mphunzitsi wamkulu wa timu ya dziko la Malawi, RVG adziwa za tsogolo lake maka ngati apitilize kuphunzitsa timuyi Lachisanu.
Nyasa Big Bullets are the champions of 2019 EcoBank Charity Shield after beating Wanderers by a goal to nil.
Next game is Wanderers vs Bullets, Blantyre Derby the finals of EcoBank.
Post #ecobankcharity updates tiuzeni za#ecobankcharity
We have now posted Saturday results and Sunday fixtures. Tayika mmene magemu a lero athera ndi mmene akhalire mawa.
Football fans in Malawi in particular those in Blantyre will tomorrow watch second Blantyre Derby in Ecobank Charity Shield. This comes after the two teams won their first games in the competition.
Gate Charges
Open Stands: K2500 MBC Stands: K4000 Covered Stands: K6000 VIP Stands: K10000
Country's top soccer analyst, Charles Nyirenda has faulted Flames Head Coach, RVG for the teams failure to qualify to Afcon.
Football Association of Malawi (FAM) is yet to say weather it will renew RVG's contract or no.
This follows the expire of RVG contract at the end of this week.
Mphunzitsi wa Wanderers wati kubwera kwa osewera kuchoka ku timu ya dziko lino kwa onjezera mphamvu pomwe akukonzekera masewero amu Eco Bank Charity Shield kumathero a sabata ino.
Timu ya Nyasa Big Bullets yati zokonzekera zake pa masewero amu Eco Bank Charity Shield zikuyenda bwino. Mphunzitsi wa timuyi, Calisto Pasuwa wati osewera akulimbikira ndipo akuonetsa chidwi chozapamba.
Matimu omwe atenge nawo gawo mu mpikisano-wu CHAKA chino; Nyasa Big Bullets, BE FORWARD Wanderers, Blue Eagles and Masters Security.
Posted check on fixtures
Bungwe loyendetsa masewero a mpira mdziko muno la Football Association of Malawi (FAM) lati zokonzekera zonse za Eco Bank Charity Shield zatha tsopano. Akuluakulu a FAM atsimikiza izi.
That's great! The fixture you have posted has the same kickoff time.
Mene ma tikiti a masewero-wa akugulitsidwira; Open Stands: K1,000 + Vital Water, MBC Stands: K2,000 + Vital Water, Covered Stands: K3,000 + Vital Water, VIP Stands: K5,000 + Vital Water.
Bungwe loyendetsa mpira mdziko muno lero lichititsa msonkhano wa wolemba nkhani pomwe anene kampani ina yomwe azigwira nayo ntchito. Msonkhano-wu uchitikira ku Chiwembe ndipo uyamba 10 koloko mawa uno.
Timu ya Zambia yafika mdziko muno pomwe mawa ikuyembekezeka kusewera ndi timu ya chisozdera ya dziko lino, Malawi U23.
Masewero-wa azachitikira pa bwalo la Kamuzu mawa mu mzinda wa Blantyre.
Yamikani Chester afika lero mdziko muno kuchokera ku USA komwe akusewera mpira wake.
Chester akuyembekezeka kuchita nawo zokonzekera ndi timu ya Flames yomwe ili mu camp pakadali pano.
Miracle Gabeya komanso Nenani Juwaya alephera kuyamba nawo zokonzekera ndi timu ya Flames Lolemba kaamba koti ndi ovulala.