Mphunzitsi wa timu ya mpira ya dziko la Malawi, Meck Mwase, wawina magemu ambiri mu chaka chimodzi kuposa aphunzitsi ena, yatero The Nation.
Kuwerengera magemu 100:
Mwase wawina 33 kuluza 20; RVG anawina 9 kuluza 38; Mtawali anawina 31 kuluza 40; Chimodzi anawina 25 kuluza 38. www.mwnation.com
Meck mwase amatha nd dolo, coach azikhala olimbika zinthu zimayenda bho
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores