Timu ya Moyale Barracks yalengeza kuti yasiyana ndi anyamata atatu omwe amatumikira timuyi.
Iwo ati Tizah Nyirenda, Dan Kumwenda ndi Mphatso Kasonga sakhalanso mbali imodzi ya timuyi.
Iwo awathokoza osewerawa pokhala ndi timuyi ndipo awafunira zabwino pamene akusakasaka kwina kopita.
📷: Mphatso Kasonga
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores