Ndalama zokwana K154 million ndi zomwe zapezeka pa masewero omwe matimu a Mighty Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets anakumana.
Pa bwalo la Kamuzu panadzadza koopsa moti malo ena omwe samakhalidwa ku akhala anthu omwe amafunitsitsa kuti awonere masewerowa.
Timu ya Wanderers ndi yomwe yapambana masewerowa 1-0 ndi chigoli cha Blessings Mwalilino.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores