AKATAKWE AJA AFIKA!
Osewera atimu ya Flames afika mdziko lino kuchokera ku Mali komwe anakagonja 3-1 ndi timu ya Burkina Faso.
Osewera onse afika pa ma bwalo andege a Chileka komanso Kamuzu International ndipo tsopano akubwerera ku matimu awo komwe amatakasa mpira mododometsa!
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores