CRECK YASAINA CHAOMBA
George Chaomba, katswiri wa mpira osewera kutsogolo wa zaka 24, lero wabwera ku team ya Creck Sporting Club.
Katswiriyu yemwe adapita ku team ya Silver Strikers chaka chatha, mwezi wa August kuchokera ku Mighty Tigers, wasayina m'gwirizano wa zaka ziwiri ndi team ya Creck Sporting club.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores