APHUNZITSI ALEMBERE NTCHITO KU WANDERERS
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers kudzera mwa akuluakulu atimuyi apanga chiganizo choti omwe akufuna ntchito yauphunzitsi ku Mighty Mukuru Wanderers achite kulembera kaye kalata.
Mkulu woyendetsa ntchito za timuyi, Roosevelt Mpinganjira, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati timuyi idzachita kusankha pa omwe alemberawa kuti atenge ntchito.
Izi zikudza kamba ka kuchoka kwa mphunzitsi wawo, Mark Harrison ndipo timuyi yachotsanso onse omwe amaphunzitsa kutimuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores