Zokonzekera za masewero otsanzikana ndi wosewera wakale wa Wanderers komanso Malawi, Joseph Kamwendo, ati zafika pa chimake.
Joseph Kamwendo watsimikiza izi poyankhula ndi Owinna.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores