Akuluakulu oyendetsa ligi ya Chipiku sabata ino akhala ndi mkumano ounikira momwe ligiyi inayendera chaka chatha.
Pa mkumano-wu mwa zina akambirana zinthu zomwe akufuna kufikira chaka chino.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores