Emmanuel Zoya akhala mmodzi wa othandizira aphunzitsi pa ndondomeko ya ana achisodzera ya mpira m'mudzi mwathu under 14.
Yemwe akuyendetsa ndondomeko-yi, Chimango Munthali, watsimikiza za izi.
Zoya azigwira ntchito limodzi ndi Abas Makawa komanso Patricio Kulemeka.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores