Timu ya Flames ikumana ndi timu ya Ethiopia pa masewero apaubale omwe ayikidwa pofuna kukonzekera masewero opitira ku African Cup of Nations.
Timuyi idzakhala koyenda mu masewero onse pa 06 June 2026 ndipo masewero ena adzakhalapo pa 09 June 2026.
Bungwe la Football Association of Malawi ndi lomwe lakwanitsa kupeza masewero apaubalewa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores