Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
"BULLETS NDI TIMU YABWINO KOMA SICHIOPSEZO KWA IFE" - KAJAWA
Mphunzitsi watimu ya Bangwe All Stars, Trevor Kajawa, wati masewero atimu yake ndi FCB Nyasa Big Bullets atha kukhala chiyambi cha zinthu zabwino pomwe ngati angapeze zotsatira zabwino akhale akusintha pa mapointsi awo.
Iye amayankhula patsogolo pa masewerowa omwe aseweredwe pa bwalo la Kamuzu lachinayi ndipo wati timu yake yakonzeka bwino kuti mwina ichite bwino.
"Akhala masewero ovuta kwambiri poti Bullets ndi timu yabwino kwambiri koma sichiopsezo kwa Ife, kutengera pomwe Ife tili paja ndi poyipa nde tikufunikira kuti tiyambe kutolera mapointsi kuti tiyambe kusuntha nde masewero awa atha kukhala chiyambi cha zabwino." Anatero Kajawa.
Iye anati masewero omwe anagonja 1-0 ndi Mighty Mukuru Wanderers mu chikho cha Airtel Top 8 ndi osiyana ndi a lero poti zolinga zinali zosiyana kwambiri ndipo lero ayesetsa kuti apambane.
Timuyi ili pa nambala 15 mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 12 ndipo akusiyana mapointsi asanu nd
Bullets 2 : 1 Bangwe π₯π₯π₯
CAF FRUSTRATES BULLETS
FCB Nyasa Big Bullets says they are frustrated with the Confederation of African Football after the continent's mother body's failure to respond to the team's appeals since last month.
The People's team team wrote the Association to appeal against poor officiation the team faced in Zambia when they lost 2-0 to Red Arrows in the second leg of the Preliminary round of the CAF Champions League last month.
A Libyan referee awarded the home team a penalty kick where there was no contact and also denied the visiting team two penalty kicks that made the team to write the Association.
Meanwhile, Chief Executive Officer at the team, Albert Chigoga, has confirmed that CAF is yet to respond to their appeal and that they have left the issue while frustrated with the Association.
The 2-0 defeat was enough for Red Arrows to progress into the next round 3-2 on aggregate where they faced the holy water of TP Mazembe which beat them 0-2 at home and awaits the second leg in D
FLAMES DROPS 8 STEPS DOWNWARDS IN FIFA RANKINGS
Malawi National Football team are now on position 133 on the latest World FIFA rankings following poor run of results in the recent African Cup of Nations Qualifiers in September.
According to what we have seen on 19th September 2024, the Flames have moved from number 125 to 133 on the World rankings.
The team lost 2-3 to Burundi at home before suffering another 3-1 against Burkina Faso on 5 and 10 September respectively.
Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
CHIKWATA STARS AS BANGWE SODOMIZE BULLETS
By Hastings Wadza Kasonga Jr
TNM Super League struggling side, Bangwe All Stars, has produced a rare moment as they picked their third win of the season to grant FCB Nyasa Big Bullets their third defeat of the season in a 0-1 away win at the Kamuzu Stadium on Thursday afternoon.
Forward Clever Chikwata was voted the player of the match after scoring the winner to deny any hope for Bullets to fight for the League as the new coach, Trevor Kajawa guided the team to his first win in the League on his first match.
After the game, Kajawa was happy with the win saying his boys worked hard in order to find the win.
He said: "It was through hard work, my boys never gave up until they fought hard to find that goal. We narrowly lost by Mighty Mukuru Wanderers last Sunday with a penalty goal and that game had gone, we talked to each other to fight so that we get the points.
KB YAFIKA PA NAMBALA YACHITATU
Nkhonya yobwenzera yawawa pomwe timu ya Kamuzu Barracks yakwanitsa kugonjetsa timu ya Chitipa United 2-0 pa masewero omwe anaseweredwa pa bwalo la Nankhaka kuti ibwenzere chipongwe chomwe yakhala ikulandira.
Timuyi inagonja 4-1 mchigawo choyamba ndipo inabandulidwanso 2-0 mu chikho cha Airtel Top 8 lamulungu lathali koma zigoli za Samuel Chiponda ndi Gregory Nachipo zathandizira kutengera timuyi pa nambala yachitatu mu ligi.
Mphunzitsi wamkulu, Charles Kamanga, wati ndi wokondwa kamba Ka chipambanochi poti chikumakhala chosowa mu ligi.
"Anali masewero abwino kwambiri anyamata analimbikira kuti tipeze chipambano chifukwa Chitipa United ndi timu yabwino kwambiri koma tinayesetsa kuti tichite bwino chifukwa takhala tisakuchita bwino." Anatero Kamanga.
Iye anati chipambano chawo chakhala chofunikira chifukwa akwanitsa kusuntha mu ligi.
Timuyi ili pa nambala yachitatu mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 31 pa masewero 20 omwe yasewera mu ligi.
"CHIGAWO CHACHIWIRI ASEWERA NDI MA DOTOLO" - NYAMBOSE
Mphunzitsi watimu ya Chitipa United, Christopher Nyambose, wadandaula kuti mchigawo chachiwiri cha masewero awo, mpira unayima kwambiri pomwe madotolo amangokhalira kulowa mu bwalo kuti athandize osewera a Kamuzu Barracks.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 2-0 ndi timu ya KB pa bwalo la Nankhaka lachinayi masana ndipo wayamikira anzawowa kamba kokwanitsa kuwagonjetsa.
"Anali masewero abwino kwambiri tinayamba bwino koma timadziwa kuti anzathuwa abwera molimba kwa Ife chifukwa tawagonjetsako kawiri motsogozana nde tiwayamikire kuti achita bwino." Anatero Nyambose.
Iye anati timuyi inakwanitsa kusewera mu chigawo choyamba ndi anzawowa pomwe mchigawo chachiwiri kunachuluka kumenyera mpira panja komanso kugwaigwa.
Timuyi yataya mwayi wotuluka ku chigwa cha matimu omwe akhonza kutuluka mu ligi pomwe ili ndi mapointsi okwana 17 pa masewero 20 omwe yasewera.
Zamadolo
"THERE'S NO SMALL TEAM AGAINST BULLETS" - PASUWA
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Kalisto Pasuwa has admitted that it is more easy to prepare when playing against fellow big teams in Malawi than playing against the so-called small teams as their players up their games to impress against big teams.
He said this ahead of the team's match against Bangwe All Stars on Wednesday at the Kamuzu Stadium in the TNM Super League and said they need to change their mindset in order to get the better over the relegated threatened side.
"We are playing against Bangwe but again I will come again us is Bullets, it's mindset to say we are meeting Bangwe as we are saying to say Bangwe is struggling there's no team that struggled when playing against Bullets and even if it is a social team they will make you run. They will make you see that we are also there to play football here against one of the biggest teams in the country so we need also us to raise up in order for us to be picking up points." Sa
Nyasa big bullets mighty mukulu wanderers
"SITINATULUKIRETU MWINA NDI OYIMBIRA ABWINO TIDZAPAMBANA" - BUNYA
Mphunzitsi watimu ya Premier Bet Dedza Dynamos, Andrew Bunya, wati timu yake ilinso ndi mphindi zina 90 zomwe timuyi ikhonza kumenyera nkhondo kuti ipitilire mu mpikisano wa Airtel Top 8 pomwe ngati atakumana ndi oyimbira abwino atha kudzatulutsa Silver Strikers.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 4-1 ndi timu ya Silver Strikers pa bwalo la Silver lachitatu ndipo wati timu yake sinatulukebe mu mpikisano.
"Tili ndi mphindi zina 90 ku Dedza zoti titati takonza mavuto athu tikhonza mwina kukachita bwino, sitinatuluke mwina titha kukakumana ndi oyimbira abwino omwe akakwanitse kuyimbira masewero athu kenako ndi kufika mu ndime ina bwinobwino." Anatero Bunya.
Iye anadandaula ndi chigoli chachiwiri chomwe Silver inapeza ATI poti mpirawo unaponyedwa mmalo olakwika ndipo masewerowa anayimako kwa mphindi zingapo pofuna kuti chigolichi chikanidwe.
Opambana pakati pa matimu awiriwa adzakumananso ndi opambana pakati pa
Hy
CIVIL YAFIKA PA NAMBALA YACHISANU
Timu ya Civil Service United yasuntha pa ndandanda wa matimu mu ligi ya TNM pomwe tsopano yafika pa nambala yachisanu mu ligi kutsatira kulepherana 0-0 ndi timu ya MAFCO FC pa bwalo la Civo lachitatu.
Timuyi inali ndi mipata yochuluka yoti ikanatha kugoletsa makamaka mchigawo chachiwiri koma anyamata awo Christopher Gototo ndi Muhammad Biason analephera kuti agoletse mipatayi.
Mphunzitsi watimuyi, Abbas Makawa, anavomereza kuti timu yake sinasewere bwino mmasewerowa.
"Anali masewero ovuta kwambiri, sitinayambe bwino nde timayesa kuti anyamata mwina azitolera mphindi zikamapitabe koma tivomereze kuti sitinasewere bwino. Tinali ndi mipata ingapo yoti tikanatha kupeza zigoli koma taphonya ndithu, tiyang'anabe chitsogolo." Anatero Makawa.
Timuyi tsopano ili ndi mapointsi okwana 28 pa masewero 20 omwe yasewera ndipo yadumpha manambala atatu kuti ifike pa nambala yachisanu mu ligiyi.
"TIMASEWERA NDI TIMU YABWINO" - MZUNGA
Wachiwiri kwa mphunzitsi watimu ya MAFCO, Jimmy Mzunga, wati timu yake yakanika kuchita bwino pa masewero awo ngakhale kuti amafunitsitsa kupambana kamba koti amasewera ndi timu yabwino.
Iye amayankhula atatha masewero omwe afanana mphamvu 0-0 ndi timu ya Civil Service United pa bwalo la Civo lachitatu ndipo iye wati wavomereza zotsatirazi.
"Anali masewero abwino kwambiri ndipo tinabwera kuti tidzapeze chipambano komabe zativuta timasewera ndi timu yabwino komabe point koyenda ndi yabwinobwino tiyesetsa kuti tikonze mavuto omwe tawaona kuti mmasewero otsatira tidzachitenso bwino." Anatero Mzunga.
Timuyi tsopano yafika pa nambala yachisanu ndi chiwiri (7) pomwe ili ndi mapointsi okwana 27 pa masewero 20 omwe yasewera mu ligi.
"TIKATEMBENUZA ZOMWE ANTHU AKUGANIZA" - BUNYA
Mphunzitsi watimu ya Premier Bet Dedza Dynamos, Andrew Bunya, wati timu yake ikuyenera mwanjira ina iliyonse kuchita bwino mu masewero ake akoyenda ndi Silver Strikers mu ndime ya matimu asanu ndi atatu a Airtel Top 8 kuti isadzakhale ndi phuma posewera pakhomo mmasewero achibwereza.
Iye amayankhula patsogolo pa masewerowa omwe ali pa bwalo la Silver lachitatu masana ndipo wati iwo akonzeka kwambiri kuti atembenuze zimene anthu akuganiza pa masewerowa.
"Akhala masewero ovuta kwambiri tikudziwa till koyenda nde tikufunikira kuti masewero amenewa tidzachite bwino kwambiri kuti tizichepetsere phuma lomwe tidzakhale nalo pa kwathu nde ndi masewero ovuta koma tiyesetsa." Anatero Bunya.
Iye anati Silver ndi timu yabwino kwambiri yomwe zotsatira zikumawakhalira bwino akasewera masewero awo koma masewero amu chikho amakhala osiyana kwambiri.
Matimuwa adzakumana mmasewero achibwereza ku Dedza ndipo popambana pa masewero awiriwa adzakumana ndi o
"WE NEED TO USE THE HOME GROUND ADVANTAGE" - MPONDA
Silver Strikers head coach, Peter Mponda, says his team needs to win with a convincing margin so that they have lesser job in their return match of the Airtel Top 8 Quarter finals as they are playing at home.
He said this on Tuesday ahead of Wednesday first leg match against Premier Bet Dedza Dynamos at the Silver Stadium and said he knows the match would be tough.
"It is going to be a tough game, Dedza is playing away so they will come more defensive so that they don't concede or concede less but we have players who know how to handle those situations, we are playing at home we need to win convincing." Said Mponda.
He further said that Airtel Top 8 Championship needs just three games to grab it so every team will work hard in order to win it.
The return leg will be played between these two teams at the Dedza Stadium with the winner progressing to the semi finals to face the winner between Mighty Mukuru Wanderers and Bangwe All S
KB ROPES IN TEMWA
The Yellow Submarine have taken on board coach Temwa Msukwa as First Assistant Coach (FAC)effective September 16.
There is minor shakeup in KB technical panel. Denis Kambewa who was FAC is now Second Assistant Coach (SAC) replacing Blessings Kawanga who is on other duties . Charles Kamanga remains HC
Temwa is well versed with KBFC philosophy having worked as interim HC and AC respectively. His main task is to bring the team back to glory .
βWe as KB ,dismayed with the current performances of the Yellow Submarine, resoluted to take Temwa on board to help rejuvenate the team having considered several factors , commented KB General Secretary Albert Midian.
Temwa has already started working full throttle and will be in the dug out on Thursday afternoon against resilient Chitipa at Civo.