Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
"I AM DISAPPOINTED WITH THE DRAW" - BUNYA
Premier Bet Dedza Dynamos head coach, Andrew Bunya, said he was disappointed for picking a point against Chitipa United on Sunday saying home games are very good to be won.
He said this after playing a goalless draw with Chitipa United at the Dedza Stadium and said the game was hard for them as the visitors dominated them.
"It was a tough game, our friends dominated us mostly in the first 45 minutes which was not good for us because we kept on creating chances but we missed, I think at home we need to win games and this was just bad, I'm disappointed." Said Bunya.
He said collecting 8 points in their 7 games is very bad as they need to do better in their games so that they do well in the League.
Dynamos are 10th on the table with 8 points from their opening 7 games having won once, lost once and drawn five times
Tumizilani pa 0981658760
"KODI AWA NTCHITO AMAPHUNZIRA KUTI? MUSANDITOLE MKAMWA" - KAUNDA
Mphunzitsi watimu ya Karonga United, Oscar Kaunda, wati oyimbira awononga mpira mmasewero omwe timu yake yalepherana 0-0 ndi Civo United lamulungu.
Iye amayankhula atatha masewerowa mokwiya kwambiri ndipo wati samafuna kuyankhulapo za oyimbira koma tsopano zamukwana.
"Nokha mwaona mmene amayimbilira Kodi awa ntchito amaphunzira kuti? Sindimafuna kuyankhula za oyimbira ngati mmene ndinachitira ku Blantyre kuja koma mwaona sizampira izi." Anatero Kaunda.
Timu ya Karonga ili pa nambala 9 ndi mapointsi asanu ndi atatu (8) pa masewero asanu ndi awiri (7) omwe Iwo asewera.
"MWINA KUKANAKHALA VAR ZIKANAGWIRA" - MAKAWA
Mphunzitsi watimu ya Civo United, Abbas Makawa, wati masewero awo ndi Karonga United amayenera kupambana koma ziganizo za oyimbira zathandizira kuti asachite bwino.
Iye amayankhula atatha masewero omwe afanana mphamvu 1-1 ndi Karonga United ndipo wati anyamata ake anasewera bwino kungoti oyimbira wawapweteka kwambiri.
"Mwina poti ndi anthu koma Kwa anzathu amakhala ndi VAR komabe nzodabwitsa kuti wapereka yellow card kuti wathu wagwetsedwa mu box kenako akukapereka mpira woponya pansi nde sizinayende." Anatero Makawa.
Timu ya Civo ili pa nambala 11 mu ligi pomwe yatolera mapointsi asanu ndi atatu (8) pa masewero asanu ndi awiri (7) omwe yasewera.
"POINT IMODZI KOYENDA NDI YABWINO" - KADZUWA
Mphunzitsi watimu ya Chitipa United, McNerbert Kadzuwa, wati timu yake yakanika yokha kupambana masewero awo komabe wati kutenga point imodzi asangalala.
Iye amayankhula atatha masewero omwe afanana mphamvu ndi Dedza Dynamos 0-0 ndipo wati anyamata ake asewera bwino kwambiri ndipo anangokanika kupeza chigoli.
"Anali masewero abwino ndipo tasewera bwino kwambiri koma kungoti mwayi wopeza chigoli sunapezeke komabe sizinayipe chifukwa kupeza point imodzi kuyenda sizophweka nditha kunena kuti tasangalala." Anatero Kadzuwa.
Iye watinso kutolera mapointsi asanu pa masewero asanu ndi awiri omwe asewera sizinayipe kwambiri poti mapointsi akuvuta kwambiri mu ligi ndipo wathokoza anyamata ake poti akugwira ntchito yabwino.
Chitipa United ili pa nambala yachikhumi ndi chinayi (14) pomwe ali ndi mapointsi asanu (5) pa masewero asanu ndi awiri (7).
"ZINTHU SIZIKUONEKA BWINO" - MSUKWA
Mphunzitsi wogwirizira kutimu ya Bangwe All Stars, Mapopa Msukwa, wati ayesetsa kukonza malo osiyanasiyana kutimuyi kuti iyambe kuchita bwino Lori zinthu sizikuoneka bwino.
Iye amakamba izi atagonja 1-0 pakhomo ndi timu ya MAFCO ndipo wati zinthu zikuvuta kwambiri koma ayesetsa kugwiragwira kuti mwina ziyendeko.
"Sizikuoneka bwino zinthu. Tiyesetsa kuwakonzabe anyamatawa kuti mwina tiyambe kuchita bwino chifukwa tikuvutika nde sizikuoneka bwino." Anatero Msukwa.
Timu ya Bangwe ikadali pa nambala 15 mu ligiyi pomwe ili ndi mapointsi atatu okha atafanana mphamvu katatu ndi kugonja kanayi mu ligi ya 2024.
"TIMANGOFUNIKIRA CHIPAMBANO BASI" - MZUNGA
Wachiwiri kwa mphunzitsi watimu ya MAFCO, Jimmy Mzunga, wati timu yake imangofunikira kungopeza chipambano ndipo tsopano ayamba kuchita bwino kwambiri mu ligi.
Iye amayankhula atatha masewero omwe apambana 1-0 ndi timu ya Bangwe All Stars lamulungu ndipo wati tsopano timuyi yanyamuka.
"Tachipeza chipambano chomwe timachifuna panopa nde tinyamuka chifukwa timangofunikira chipambano ngati ichi basi." Anatero Mzunga.
Timuyi yatuluka mu chigwa cha matimu otuluka mu ligi pomwe ali pa nambala 13 ndi mapointsi asanu ndi imodzi (6) pa masewero asanu ndi awiri (7) poti apambana kamodzi, kugonja katatu ndi kufanana mphamvunso katatu.
MPONDA HAILS THE BANKERS AFTER NOMADS WIN
Silver Strikers head coach, Peter Mponda, was left happy with the performance of his players after dominating the Mighty Mukuru Wanderers to beat them 2-0 on Sunday afternoon at the Silver Stadium.
Mponda said after the match that his boys should receive more for their untiredness in the game and getting the goals to secure the win.
"A massive performance from the boys they played very well from the first whistle up to the last, we could lose the ball but they were quick to recover then we got the goals, credit to the boys ." Said Mponda.
He further said things are quite going well for the Bankers but they should not be carried away as it is only 7 games with 23 to wrap up the season.
The Bankers have opened a 6 point gap in top of Second placed, FCB Nyasa Big Bullets as they have 19 points from 7 games this season.
Gokeepers
"WE DID NOT PLAY WELL" - MWASE
Mighty Mukuru Wanderers deputy coach, Meke Mwase, said his team deserved to lose against Silver Strikers as they did not play well in every department of the match.
He said this after their 2-0 defeat at the Silver Stadium and said even the changes they made could not change anything because they were still second on the ball.
"I think we didn't play well today we failed to create chances and we were second on the ball so that's why we lost. We thought the chances would make a huge impact in the game but to no avail so it's a painful defeat." Said Mwase.
The Nomads missed a chance to move up to second as they have remained Fourth on the log table with 12 points from 7 games they have played this season.
Silver 2 wanderers 1
Noma 2 silver 1
Silver 1-0 Noma
Wanderers 2-1silver strikers
"WE ARE READY TO PICK THREE POINTS" - MWASE
Mighty Mukuru Wanderers deputy head coach, Meke Mwase, said his team is more than ready to face Silver Strikers and would like to work hard so that they collect maximum points in the match.
He said this ahead of the match at the Silver Stadium and said there's no exact format on how to play these big matches but they have prepared for a win this afternoon.
"There's no proper formula for these games but what we are looking forward is a win as my boys are well prepared. We faced them recently in the Kamuzu Cup but that does not give the proper overview of today's match because these games are hard." Said Mwase.
The Nomads are on position four and a win will take them up to second, a point behind the Bankers as they have 12 points from 6 games.
"BULLETS, SILVER, WANDERERS GAME DONT DECIDE THE LEAGUE" - MPONDA
Silver Strikers head coach, Peter Mponda, said the games involving Silver Strikers, FCB Nyasa Big Bullets and Mighty Mukuru Wanderers do not decide the League as a team needs to win all matches.
He said this ahead of the team's match with Mighty Mukuru Wanderers at the Silver Stadium on Sunday and said this was proven last season when the team lost the league despite not losing to Bullets.
"I think these games do not decide the League as we witnessed last year, we did not lose to Bullets but still failed to win the League because we lost to some smaller teams." Said Mponda.
Ahead of the match, he said his team is ready for the match and are already motivated to do well in order to safeguard their top spot in the League.
The team are on position one with 16 points from 6 games games having won five times and drawn once.
"NDE CHOKHALIRA NDI OYIMBIRA NDI CHANI?" - CHIRWA
Mphunzitsi watimu ya FOMO, Gilbert Chirwa, wati timu yake yagonja kamba koti oyimbira amawakondera anyamata a Creck Sporting Club ndipo sanayimbire bwino.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 1-0 pa bwalo la Civo ndipo wati timu ya Creck inayamba kuchedwetsa mpira mu chigawo choyamba chomwe koma oyimbira samachita kalikonse.
"Analidi masewero a msinkhu wathu koma masewerowa avuta chifukwa cha anzathu oyimbira. Creck inayamba kuchedwetsa mpira mchigawo choyamba, achinya chigoli chabwino koma kungotero nde oyimbira osawaletsa komanso kumangotiyimbira chilichonse nde zinawapatsa mphamvu a Creck ndikufooketsa anyamata athu." Anatero Chirwa.
Iwe wati timu yake yaonetsa kuti ili tsopano bwino ndipo anangovutika poti anaphonya mipata yochuluka mchigawo choyamba.
FOMO ili pa nambala 12 pomwe ili ndi mapointsi 7 pa masewero asanu ndi awiri (7).
"WE WILL COME BACK TO WHERE WE BELONG" - NGINDE
Creck Sporting Club head coach, Macdonald Mtetemera, said his team will soon be one of the best teams in the league as he just finalizing the correction of problems at the team.
He spoke this after recording a 1-0 win over FOMO FC and said he knew the game would be tough but happy to have collected maximum points.
"I knew it would be a tough game because we haven't been good in the past three games but I told them let's score then if we manage it and not score again it's fine so it happened, we are so far in right track and soon we will be back to where we were." Said Mtetemera.
The team have moved up to number 8 in the League as they have 10 points from their seven opening games this season.
"NDAKHUTITSIDWA NDI POINT IMODZI" - KAMANGA
Mphunzitsi watimu ya Kamuzu Barracks, Charles Kamanga, wati wakhutira ndi kutenga point imodzi chabe kutengera ndi kuvuta kwa masewero komanso poti akuchoka kogonja ndi Mzuzu City Hammers sabata yatha.
Iye amayankhula atatha masewero omwe afanana mphamvu 0-0 ndi Moyale Barracks ndipo wati akukhulupilira kuti masewero alinkudza akhale akupeza chipambano.
"Anali masewero ovuta kwambiri chifukwa anzathuwa anabwera movuta kwambiri ifenso tinali bwino koma mipata yomwe tinapeza tinaphonya nde tikuchokera kogonja apa tafanana mphamvu ndekuti sabata inayi tidzapambana koma point imodzi ndakhutira." Anatero Kamanga.
Iye wati akhale akukonza mavuto awo omwe awaona mmasewerowa ndipo sabata ya mawa adzachita bwino.
Timuyi ikadali pa nambala yachisanu (5) mu ligi pomwe ili ndi mapointsi 12 pa masewero 7 yomwe yasewera pomwe yapambana katatu, kufanana mphamvu katatu ndi kugonja kamodzi.
"WE NEED TO SHARPEN OUR FRONT LINE" - MWANSA
Moyale Barracks head coach, Prichard Mwansa, said picking a point away from home is not bad but they prepared for three points only that they are missing a lot of chances.
He said this after the team played a goalless draw with Kamuzu Barracks at the Aubrey Dimba Stadium and said he will look for solutions so that they stop missing a lot of chances.
"We played very well but unfortunately that we got more chances which we missed but I think it's becoming a serious problems so we gonna look them out during but all in all it was a tough match but an away point is good as well." Said Mwansa.
The Lions of Kaning'ina are seventh on the log table as they have 9 points from 7 games in the League after winning twice, drawing three times and losing twice this season.
"WE HAD A PENALTY BUT THE REF SAID NO" - CHIRAMBO
Mzuzu City Hammers head coach, Elias Chirambo, said his team was left frustrated by the referee for not giving them a penalty and that made them lose their second match of the season.
He said this after suffering a 2-0 loss over FCB Nyasa Big Bullets and said the team also had a failure in tactics in the second half and that proved to be a blow for the Mzuzu based team.
"I think we were upset in the first half because of the referee, we had penalties but the referee couldn't whistle but all in all we have lost them and we will look forward." Said Chirambo.
The team remain in the top three as they have 13 points from their 7 games played this season and have lost all two matches they have played at the Kamuzu Stadium.
PASUWA SLAMS DEFENDERS FOR DRIBBLES AT BACK
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Callisto Pasuwa, slammed what the team's defenders were doing by making dribbles at the back of the team and said this could have hurt them in the game.
This comes after the team's winning 2-0 against Mzuzu City Hammers on Saturday that saw Colin Mujuru substituted on 41st minute and said it's bad to underrate teams.
"We underrated the team you could see center back dribbling at the back, we need to respect these team remember they are second in the league we are playing then trying to funny in front of them they will punish you but the good thing is that we settled well and we got goals that we needed and we took the three points. Said Pasuwa.
He further said he is the process of building a team as he looks for combinations of players who were bought, promoted and old ones at the team.
The People's team jumped into position 2 after collecting 13 points from 7 games this season.
SILVER MEN REJECT WOMEN'S PROPOSAL
Silver Strikers has said no to a proposal made by the National Women's Football Association to allow the final of the Goshen National Women's Football Championship be played as a curtain raiser in the Bankers TNM Super League match against Mighty Mukuru Wanderers on Sunday.
According to reports that have reached our publications, the Bankers are not interested in the deal which could see the game be moved from Silver Stadium to Bingu National Stadium.
The Bankers would want to stick to play the match at the Silver Stadium and that they have rejected the call made by the Association's chairperson, Adelaide Migogo.
The Association thought it wise to make the game played earlier before the Bankers game so that they hold spectators that would abscond the final for the TNM Super League block buster match.
We are yet to hear from Migogo's reaction to the matter.
"WE NEED TO TREAT HAMMERS WITH RESPECT" - PASUWA
FCB Nyasa Big Bullets head coach, Callisto Pasuwa, has also warned his charges against underrating Mzuzu City Hammers saying the team is on its best making them to sit second in the League this season
He said this ahead of their meeting on Saturday at the Kamuzu Stadium and said they need to treat Hammers with respect so that they win the match.
"And again as I always preach, it's our mind that we can make us will games. If we treat Mzuzu City Hammers as Hammers we can call it then we can end up losing points so we need to be positive on our approach and everything then we will say we have won the match."
"There's no small team and for that Mzuzu City Hammers to be second it means something else, this season they have been playing good football and also we need to treat them with respect so that we can come up with all points." Said Pasuwa.
Meanwhile, he said that Ernest Petro had returned to the team's squad whilst others who were
3 bullets 0 mzuzu
CAF YAKHULUPILIRA AMALAWI ATATU
Bungwe loyendetsa mpira mu Africa la Confederation of African Football (CAF) lapereka maudindo kwa a Malawi atatu pa mpikisano wa masukulu amu Africa omwe uyambe pa 21 May ku Zanzibar.
Atatuwa ndi mkulu woona za mipikisano ku bungwe la Football Association of Malawi, Gomegzani Zakazaka komanso oyimbira awiri, Faith Gondwe komanso Wyson Mustafa, ndipo akagwira ntchito ku mpikisanowu.
Iwo adalinso pa mpikisano wa COSAFA wopitira ku mpikisano wa Africa yonse ndipo akuyembekezeka kunyamuka lero kulowera ku Zanzibar komwe mpikisanowu ukathe pa 24 May 2024.
SAPOTA WA FOMO WAMENYEDWA PA CIVO
Wachiwiri wa wapampando wa komiti ya ochemelera a timu ya FOMO mchigawo chapakati, Peter Malata ali ku chipatala komwe akulandira thandizo atamenyedwa ndi anthu omwe akuganiziridwa kuti ndi masapota atimu ya Clerk Sporting club.
Malingana ndi mlembi wamkulu wa komiti ya masapota FOMO mchigawochi, Felix Gunya, wati anthuwa anafika pa bwalo la CIVO kuzachita za zikhulupiliro zawo pamapeto a zokonzekera za timu ya FOMO, ndipo pokanizidwa kulowa mu bwaloli anayamba kumenya wachitetezo wa FOMO pamodzi ndi wapampandoyi.
Iye wati mwamwayi, wachitetezo anapeza mpata othawa ndipo tsopano ali ku chipatala.
Matimu a Creck Sporting Club komanso FOMO akumane pa masewero awo mu TNM Supa ligi pa bwalo la Civo pa nkhondo yotolera mapointsi.
Source: FOMO FC
"TIKUKAPAMBANA MWA NJIRA ILIYONSE" - BUNYA
Mphunzitsi watimu ya Dedza Dynamos, Andrew Bunya, wati timu yake ikhale ikupeza chipambano mwa njira iliyonse pomwe akhale akusewera pakhomo loweruka.
Iye amayankhula patsogolo pa masewero omwe asewere ndi Chitipa United pa bwalo la Dedza ndipo wati zokonzekera zawo zayenda bwino ndipo chatsala ndi kupeza chipambano basi.
"Zokonzekera zayenda bwino kwambiri ndipo anyamata akuoneka bwino kutengera ndi mmene akuthamangira komanso ku mbali ya ovulala nde tili okondwa ndi mmene tilili ndipo mwa njira iliyonse mawa tipeza chipambano." Anatero Bunya.
Iye anati akudalira osewera aliyense poti onse ali mu dongosolo lake ndipo malingana ndi mpikisano pakati pa anyamatawo akumasowa kuti ayambitsa ndani.
Timu ya Dedza ili pa nambala yachikhumi (10) pomwe yatolera mapointsi asanu ndi awiri (7) pa masewero asanu ndi amodzi (6) omwe yasewera.
"WE WILL FIGHT FOR A WIN" - MWANSA
Moyale Barracks head coach, Prichard Mwansa, says he expects a tough match as they face their fellow soldiers, Kamuzu Barracks but said they will play their normal game so they fight for a win.
He spoke this ahead of the match at the Aubrey Dimba Stadium in Mchinji on Saturday and said they have prepared well for the match.
"We are well prepared for this match, I know it's going to be tough because KB also plays well but we are fully determined and will fight to a win on Saturday." Said Mwansa.
He further said that the fact that they will play for their very first time at the Dimba Stadium will not affect them as they will approach the game as any other match.
The team is on position number 7 with 9 points having won twice, drawn three times and lost once in their opening 6 matches of the League.
"TAKONZA NDI PA BENCH POMWE" - NGINDE
Mphunzitsi watimu ya Creck Sporting Club, Macdonald Nginde Mtetemera, wati timu yake tsopano yakonza mavuto awo onse omwe amakumana nawo mmasewero omwe akhala asakuchita bwino ndipo akukhulupilira kuti achita bwino loweruka.
Iye amayankhula patsogolo pa masewero omwe asewere ndi timu ya FOMO pa bwalo la Civo ndipo wati akonzeka kuti akapambanepo pa masewerowa.
"Takonza monse pagolo, kumbuyo, pakati komanso kutsogolo, angakhale pa bench ndi malo nde takonzekera ndithu kuti tikatenge chipambano, tikuyenda tsopano bwino chifukwa tsopano timuyi ikukonzeka bwinobwino." Anatero Mtetemera.
Iye wati yakwana nthawi tsopano kuti awapepese masapota atimuyi ndi chipambano ndipo tsopano mwa njira iliyonse Iwo apambana.
Timu ya Creck Sporting Club ili pa nambala 11 pomwe yapambana masewero awiri, kufanana mphamvu kamodzi ndi kugonjanso katatu ndipo ali ndi mapointsi asanu ndi awiri (7).
"SITIKUTULUKA MU LIGI IFE" - MUYOMBE
Mphunzitsi watimu ya Baka City, Davie Muyombe, watsutsa zoti palibe chiopsezo kuti timu yake ituluka mu ligi poti wati agwiritsa ntchito mwayi pa masewero awo apakhomo.
Iye amayankhula atatha masewero omwe agonja 4-1 ndi timu ya Mighty Waka Waka Tigers lachinayi ndipo wati timu yawo singatuluke mu ligi.
"Kutuluka ayi aah sitingatuluke, lero zinangotivuta poti osewera ena kunalibe koma tikadzakhala pakwathu sitingamachite chonchi ndipo tidzawina pakhomo." Anatero Muyombe.
Timu ya Baka City sinapambaneko masewero aliwonse mu ligiyi chilowereni pomwe yagonja kasanu ndi kufanana mphamvu kawiri ndipo ili ndi mapointsi awiri pa masewero asanu ndi awiri.
"TIKADALI NDI NTCHITO YOTI TIKONZE TIMUYI" - MPULULA
Mphunzitsi watimu ya Mighty Waka Waka Tigers, Leo Mpulula, wati ali ndi ntchito yaikulu yoti agwire kutimuyi kuti ikhale bwino pomwe akufunitsitsa kuti achite bwino mu ligi ya 2024.
Mpulula amayankhula atatha masewero omwe apambana 4-1 ndi timu ya Baka City lachinayi ndipo wati ngakhale apambana, zambiri zikuyenera kukonzedwa.
"Anali masewero abwino poti tapambana masewerowa komabe ntchito ilipo yoti tikonze kuti timuyi izisewera bwino komanso mipata yochuluka nde tayiphonya nde komabe tikonza." Anatero Mpulula.
Iye wati kugoletsa zigoli zinayi zikuonetsa kuti zomwe akuwaphunzitsa osewera ake zikugwira ntchito komabe zina azizidziwa mochedwerapo.
Timuyi yafika pa nambala yachisanu pomwe ali ndi mapointsi khumi ndi imodzi (11) pa masewero asanu ndi awiri (7).
Two charged over illegal sale of tickets
The Blantyre Resident Magistrate court have charged two individuals, Francis Danger and Samson White, after found guilty of selling tickets in the game involving Mighty Mukuru Wanderers and Karonga United last Saturday.
The two appeared before the court on the same day after being apprehended by the police after reports that they were selling tickets on the match day despite not being accredited to do the job.
They have been charged with an offence if being found with in possession of property suspected to be stolen, in contrary to section 329 as read with section 34 of the penal code.
Meanwhile, the super League of Malawi has reminded all stakeholders that it is punishable by law to be found with matchday tickets for the elite league matches without proper procedures and may led to criminal prosecution.
Danger, aged 24, hails from Konzere Village T/A Ngabu in Chikwawa district while Samson who is aged 35 comes from Machinga District T/A St
2-1
Manoma 2 sliver0
NO SERIOUS INJURIES IN NTOPWA'S ACCIDENT
No serious injury has been recorded as 6 Ntopwa Queens players have been treated as out patients after the team got involved in a car accident as they were travelling back from Lilongwe on Tuesday night.
This has been confirmed by the team's owner and head coach, Isaac Jomo Osman who said all those who got injured have been treated at Queen Elizabeth Central Hospital on Wednesday.
"I can confirm that there are no serious injuries on our girls. They just have minor injuries. Out of the 26 girls, six had minor and have been treated as out patients and they are now at home." Wrote Osman.
Meanwhile, he went on to thank Football Association of Malawi President, Fleetwood Haiya, National Women's Football Association Chairperson, Adelaide Migogo, FAM Chairperson for the competitions committee, Hon. Felistas Dossi, their Sponsor Kukoma and all other people for their assistance after the accident.
"Thanks to all the people for being with us throughout the night up to the time we arrived home." He added.
The team's bus was involved in an accident at Lizulu in Ntcheu after the driver tried to run from a convoy by State President, Dr Lazarus McCarthy Chakwera, and landed on an ox-cart on the side of the road.
The team was coming from Lilongwe where they were knocked out of the Goshen National Women's Football Championship after a 4-0 defeat over Ascent Academy on the same day.
0-1
Four awards of same kind
Tabitha Chawinga was yesterday awarded as the best player of the 2023/24 D1 Arkema season and also got a place in the team of the season in the League at Trophees UNFP.
This comes after having a stellar performance in the season which saw her netting 18 goals and providing 10 assists despite being her debut season.
Chawinga was awarded the same awards last week by D1 Arkema and these are of another kind. In the season, Chawinga also won two player of the month awards, missed one and also missed the goal of the month award.
Her contract ends after the season which ends on Friday as PSG play Olympic Lyonnais in the D1 Arkema playoffs Championship final and has already won the Coupé de France with PSG.
In 2022/23 season, she won three awards that included the two when playing in Italy with Inter Milan.
3-0
2-0