Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Zondie ndi Ezala agawana K10,000πΈ atalosera molondolaπ― magemu 5 pa Owinnaβ½ Monday - Sunday π
Loserani magemu ambiri pa Owinna.com kuti nanunso mukhale ndi mwayi wowina ndalamazi.
Southampton have been π«ππ₯ππ ππππ to the Championship after 11 years in the Premier League
Lonk
Arsenal defenders Oleksandr Zinchenko and William Saliba are out for the rest of the season.
Zinchenko picked up a calf injury during their win against Newcastle and Saliba hasn't played since being injured on March 16.
Bungwe la SULOM lalengeza kuti masewero a Silver Strikers ndi Mighty Tigers omwe amayeneleka kukhala loweruka pa 13 May alepheleka.
Izi zili chonchi chifukwa bwalo la Bingu National Stadium izakhala ndizochitika pokonzekera tsiku la Kamuzu pa 14 May. Choncho masewerowa ayikidwa tsiku lina lomwe sananene.
Bungwe la FAM lalembera kalata Hassan Kajoke ndi nthumwi yake Ken Mvula komanso matimu a FCB Nyasa Big Bullets ndi Silver Strikers kuti lachiwiri pa 16 May, 2023 akayambe kumva za mlandu wa osewerayu.
Silver Strikers inasuma kuti Kajoke anadya ndalama zatimuyi komanso anasaina kontrakiti ndi timuyi zomwe zabwelesa mpungwepungwe chifukwa osewerayu akusewera ku Bullets pano.
Mphunzitsi wamkulu wa Silver Strikers Pieter De Jongh wayitanisidwa mkachipinda komata katimuyi kamba kosowa khalidwe.
A Jongh pamasewero anayi omwe Silver yasewera alandira ma yellow card awiri ndi red card imodzi zomwe zawakhuza akuluakulu a Silver kuti amufunse kuti chikuvuta ndichani.
Mbali ina, bungwe la oyimbira masewero ampira wamiyendo a dziko lino la National Referees Association (NRFA) lapempha Super league of Malawi (Sulom) kuti lipereke chilango kwa Pieter De Jongh.
A Jongh ati akusowa khalidwe pamene akumalimbana ndi oyimbira posagwilizana ndiziganizo zawo.
Leo Messi has won the 2023 Laureus Sportsman of the Year Award! He becomes the only footballer ever to win it twice.
Karonga united
BLULLETS NDIPAMWAMBA PA ANA ONSE AMUTNM SUPER LEAGUE AMAFUNA AKUNYIMWISEN KAYE MUDZIWE MPIRA TNM CHAKA CHINO MOTO KUTI BUU!!!!? (SADRINHO MALIKO SAUFU) WA KU NSANJE