Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
The CAF Champions League quarter-finalists:
π²π¦ Raja AC π²π¦ Wydad AC π©πΏ CR Belouizdad π©πΏ JS Kabylie πͺπ¬ Al Ahly πΉπ³ Esperance de Tunis πΏπ¦ Mamelodi Sundowns πΉπΏ Simba SC
North Africa - 6οΈβ£ COSAFA - 1οΈβ£ CECAFA - 1οΈβ£
Christopher kumwembe
Bungwe la FAM latsimikiza kuti silionjezera mgwirizano wake ndi mphunzitsi wa timu ya Flames Mario Marinica ukatha pa 30 April.
Kalata yomwe mlembi wa FAM Alfred Gunda walemba yatsindika za chikonzerochi
FAM yati izamukumbukira Marinica popanga mbiri komanso kubweletsa chimwemwe pamene Malawi inafika koyamba mu Round of 16 ku AFCON imene inaseweledwa ku Cameroon chaka chatha.
Banki ya NBS yaonjezera ndalama za chikho cha Charity Shield kuchoka pa 15 million kwacha kufika pa 20 million Kwacha.
Mkulu oyendesa ntchito za banki ya NBS, Kanele Ngwenya atsimikiza za nkhaniyi.
Matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers akuyembekezeka kukumana mu chikho cha chaka chino cha pa 9 April pa bwalo la Bingu National Stadium.
Chaka chino ndalama zomwe zitapezeke masewerowa zigwilitsidwa ntchito kuthandiza anthu omwe akhunzidwa ndi namondwe wa Freddy.
Super league will start when?
π¨OFFICIAL: Arsenal manager Mikel Arteta has been named the Premier League Manager of the Month for March 2023, his fourth time winning the award this season.
Bukayo Saka wins Premier League Player of the Month for the first time in his career.
β’ 4 games. β’ 2 assists. β’ 3 goals.
Usiku wathawu akuluakulu a Malawi Council for Sports ndi a Football Association of Malawi anali mkachipinda komwe amakambirana za tsogolo la mphunzitsi wamkulu wa timu ya dziko lino, Mario Marinica.
Mwa zina amaunikira momwe Marinica wachitira ndi Flames ndipo amvana zoti mgwilizano wake ukafika kumapeto pa 30 April mwezi wa mawa sakuyenera kupatsidwanso mgwilizano wa tsopano.
Choncho lero Football Association of Malawi ikumana ndi mphunzitsiyu kuti amudziwitse izi kuti akhoza kudikilabe kufika pa 30 April kapena atuliletu pansi udindo chifukwa sapasidwanso kontrakiti ina.
Timu ya Silver Strikers yatsimikiza kuti yasaina osewera wao wakale Atusaye Nyondo.
Nyondo amene wasewerapo mayiko a South Africa ndi Ethiopia wasaina mgwirizano wa chaka chimodzi .
The Football Association of Malawi has disclosed that the match between Malawi and Egypt grossed MK76.4 million in gate revenue.
CAF has announced the dates for AFCON 2023 competition.
The opening match is scheduled to take place on Saturday, January 13, 2024, at Alassane Ouattara Stadium in Abidjan, while the final will be played on February 11, 2024.
Bungwe lomwe limayang'anira mpira la FAM lanena kuti iwunikila bwino m'mene mphunzitsi wa Malawi wachitira kontrakiti yake ikatha pa 5 April.
A Marinica adasankhidwa kukhala mphunzitsi wa Malawi chaka chatha ndipo adasayina kotrakiti ya chaka chimodzi.
Izi zikudza pamene pali maganizo a anthu osiyanasiyana kuti mwina mphunzitsiyi apasidwe kontrakiti ina kapena ayi kutsatira kusachita bwino kwa Flames mu ndime yozigulira malo mu AFCON.
A Marinica poyankhila pankhani yakusachita bwino kwa Flames ati satula pansi udindo kufikira kontrakiti yawo itatha.
Arsène Wenger and Sir Alex Ferguson have both been inducted into the Premier League Hall of Fame.
They'll be the only managers inducted.
Here are 7 teams that have qualified for AFCON 2023 so far. The tournament is to be held in Ivory Coast, January 2024.
Ivory Coast (hosts), Morocco, Algeria, Namibia, Senegal, South Africa, Burkina Faso and Tunisia.
Herve Renard has resigned as head coach of Saudi Arabia where his contract ran until 2027.
The two-time AFCON winning coach is expected to take over the France Womenβs team.
Atipweteka, atisenda ndipo atiyalutsa: Ijipiti ya Mo Salah 4 Malawi ya Marinica 0 Zoti tiri pa chisoni sizinaoneke. Zoti tate wathu ndi m'busa sizinaonekenso. Pena kumati mwina malaya ofiyira... malawi24.com
Temwa Chawinga scores twice Scorchers striker Temwa Chawinga netted a brace as her side Wuhan Jiangda thrashed Shanghai Shengli 4-2 in the Chinese Super Womenβs Cup on Sunday.
It is her second... times.mw
Zitha Foundation takes over St. Gabriel Medicals FC St. Gabriel Medicals Football Club are expected to change its name to Namitete Zitha Football Club after securing sponsorship deal from Zitha... atlasmalawi.com
Comoros vs ivory coast
Malawi vs Egypt today
Osewera a Flames dzulo ananyanyala kuti sapitiliza zokonzekera chifukwa cha kusalipidwa.
Osewerawa amadandaula kuti sanalandire ndalama zawo masiku 10 omwe anali ku Saudi Arabia komanso masiku 5 omwe anali ku Egypt.
Izi zikudza pomwe Malawi ili ndi masewero akulu mawa mu ndime yozigulira malo ku 2023 AFCON.
Much improved second-half performance saves Malawi from humiliation Malawi National Football Team on Friday lost 2-0 away to Egypt in the 2023 Africa Cup of Nations (Afcon) first leg match played... malawi24.com
Manager Antonio Conte has left Tottenham Hotspur by mutual consent after 16 months in charge.
Cristian Stellini and Ryan Mason will take charge of their remaining 10 games in the 2022/23 Premier League season.