Vitumbiko Kumwenda wati palibe mgwirizano uli onse ndi timu ya Silver Strikers.
Izi zikutsatira zomwe timu ya Blue Eagles inalengeza kuti osewerayu ndi wa mabankers tsopano.
Ndekuti akanali ku Blue Eagles
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores