Takumana ndi vuto lamakina a banki imene timagwiritisa ntchito potumiza ndalama kwa amene alosera bwino kuposa onse. Izi zapangitsa kuti owina atatu asalandire mphoto zawo. Tiyeseranso kutumiza mawa mmamawa.
Pepani chifukwa cha vutoli.
0888218915 Osward Nakoma
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores