Osewera a Flames dzulo ananyanyala kuti sapitiliza zokonzekera chifukwa cha kusalipidwa.
Osewerawa amadandaula kuti sanalandire ndalama zawo masiku 10 omwe anali ku Saudi Arabia komanso masiku 5 omwe anali ku Egypt.
Izi zikudza pomwe Malawi ili ndi masewero akulu mawa mu ndime yozigulira malo ku 2023 AFCON.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores