FCB Nyasa Big Bullets yalengeza kuti yasaina osewera kusogolo wa dziko la Nigeria John Okafor. Osewerayu wasaina kontrakiti ya zaka ziwiri.
Okafor yemwe ali ndi zaka 22 wajoina Bullets mwaulere atayesa mwayi kwa masabata atatu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores