Kubanja la Bangwe Ngati mbali imodzi yokwanilitsa mfundo za Club licensing timu ya Bangwe All Stars lero yasayinilana mgwilizano wa chaka chimodzi ndi matimu a Bvumbwe Women's United ndi Agumbala FC.
Matimuwa sopano akhala m'manja mwa Bangwe All Stars.
Khonsolo la boma la Mulanje lavomeleza pempho la Bangwe All Stars kuti ikhonzaso kumagwilisa bwalo la Mulanje Park Stadium akakhala akusewera pakhomo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores