Timu ya Fc Botosani ya dziko la Romania yalengeza kuti yasaina katswiri otchinga kumbuyo wa dziko lino Charles Petro. Osewerayu wasaina kontrakiti ya zaka ziwiri ndi theka.
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets dzulo yalengeza kuti yasaina osewera awiri otseka kumbuyo a dziko la Kenya Clyde Senaji komanso Collins Odhiambo Okumu pa mgwirizano wa chaka chimodzi aliyense.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores