Takumana ndi vuto lamakina a banki imene timagwiritisa ntchito potumiza ndalama kwa amene alosera bwino kuposa onse. Izi zapangitsa kuti owina atatu asalandire mphoto zawo. Tiyeseranso kutumiza mawa mmamawa.
Pepani chifukwa cha vutoli.
Tiyamikile aliyese walandila panthawi yomwe munalonjeza. ZIKOMO.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores