Timu ya Silver Strikers yatsimikiza kuti katswiri wawo wakutsogolo, Chinsisi Maonga, waonjezera mgwirizano wake ndi zaka zitatu kutimuyi.
Iye akuyembekezeka kukhalabe kutimuyi kufikira mpaka mu chaka cha 2028.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores