Ndalama zokwana K113 million ndi zimene zapezeka pa bwalo la Bingu pomwe matimu a Silver Strikers komanso FCB Nyasa Big Bullets amakumana mu masewero otsegulira ligi.
Timu ya Bullets ndi imene yapambana masewerowa 1-0 ndi chigoli cha Babatunde Adepoju cha mchigawo choyamba cha masewerowa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores