BREAKING NEWS
Bungwe la Central Region Association of Malawi lapeza timu ya Ngolowindo FC ndi mlandu woti iyankhe pa nkhani yogulitsa masewero mu ligiyi.
Ngolowindo inakanika kufika pa bwalo la zamasewero kuti isewere ndi Namitete Zitha ndipo kunamveka kuti anauzidwa ndi a Kawinga FC kuti asapiteko.
Kwachema
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores