"UKAMAIMBIRA BWINO OYIMBIRA ANZAKO AMADANA NAWE" - CHIZINGA
Mmodzi mwa oyimbira omwe agwira ntchito mu zaka zapitazi, Alfred Chizinga, wayankhulapo pa nkhani yomwe Oyimbira ena aku Blantyre amadandaula kuti Mwayi Msungama akukonderedwa pomwe wati ukamaimbira bwino amadana nawe.
Iye walemba izi pa tsamba lake la Facebook ndipo wati iyenso kwakumanapo nazo zoterezi komabe anakwanitsa kupita patsogolo mpaka kuimbira Blantyre derby ka 19 opanda zosokoneza.
"U Ref wa ku Malawi, ukakhala kuti ukuyimbira bwino, ndipamene ma refs anzako amayamba kudana nawe amvekere amamukondera, amapereka ndalama kwa mabwana nanga ref ndiyekhayu😀"
"I had similar situation when I was active, ndipo nditalowa pa FIFA nawo a CAF anagundika kundipansa ma games pafupipafupi ndipo ndinawanfunsa ma Dolo komanso ma ladies omwe amalumbwalumbwawo, Kodi a CAF wa akundikondelanso?? Onse adangoyakha kuti inuyo mumatha man😀." Iye analemba chonchi.
Iye wati Msungama akuyeneradi kuimbira masewero pakati pa FCB Nyasa B
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores