NKHANI
Katswiri wa timu ya Scorchers, Tabitha Chawinga, wasankhidwa mu gulu la osewera khumi omwe asewera mwapamwamba mu sabata yangothayi mu ligi ya mpira wamiyendo koma ya amayi ku France.
Chawinga anagoletsa chigoli chimodzi komanso kuthandizira chinanso pomwe PSG inagonjetsa Lens 4-0.
Katswiriyu tsopano wagoletsa zigoli zitatu komanso kuthandizira zina ziwiri pa masewero asanu omwe wasewera kutimuyi.
Wolemba: Hastings Wadza Kasonga Jr
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores