SULOM SINAPEREKE NDALAMA KU FAM
Bungwe la Football Association of Malawi likufuna ndalama yokwana K4.7 million kuchokera ku Super League of Malawi pa ndalama zomwe zikapezeka pa masewero a Mighty Mukuru Wanderers ndi FCB Nyasa Big Bullets.
Bungwe la SULOM silinapereke ndalamazi ku FAM pomwe bungweli linasambira mmanja SULOM kamba koyika masewero aakulu pa bwalo la Kamuzu zomwe FAM imakana.
Atatha masewero, ndalama yokwana K56.4 million ndiyomwe inapezeka pa masewerowa ndipo K4.7 million zinapite ku FAM monga mmene zimayenerera.
Bungwe la SULOM silinayankhepo pa nkhaniyi pomwe mkulirano ukuchulukirabe.
Ndipo isapeleke because sulom silandila ndalama kuchoka kufam when Flam's imasewela ngakhale Fdh any cup sulom silandila kalikonse . these year we need change . nyamilandu akagwele uko chaka chino enough is enough
keep it up sulom apa mwabwera
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores