Timu ya mpira wamiyendo koma ya amayi ya Kamuzu Barracks, yalemba Technical Director wakale wabungwe la Football Association of Malawi, John Kaputa, kukhala mphunzitsi wawo.
Arnold Jere watsimikiza.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores