Katswiri wotsatira Mpira wa zamasewero, Parry Chinyama wati zikhulupiliro za mmasewero a Mpira ku Malawi sizingatitengere kulikonse ndipo wati zilibe phindu.
Iye wadzudzula zomwe FCB Nyasa Big Bullets inachita polowetsa bus mwa futa mmbuyo komanso Mighty Mukuru Wanderers pothira mkodzo pagolo la Chitipa United ngakhale kuti onse anagonja.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores