Vitumbiko Kumwenda ndi osewera wa BE FORWARD Wanderers tsopano.
Owinna itha kutsimikiza kuti osewerayu wasaina kontrakiti ndi timuyi masiku apitawa.
Osewerayu amafunidwaso ndi timu ya Silver.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores