Woimba wodziwika bwino mdziko muno, Patience Namadingo, wayamikira Gabadinho Mhango kaamba kokhala katswiri womwetsa zigoli zochuluka mu ligi yaikulu ku South Africa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores