Boma tsopano labwera poyera pomwe lati ntchito yomanga mabwalo a Bullets ndi Wanderers iyambika mu February.
Nduna ya zamasewero, Francis Phiso, yatsimikiza za nkhaniyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores