Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Nbb vs Platinum
Timu ya Nyasa Big Bullets lero inyamuka mdziko kupita ku Zimbabwe komwe akasewere masewero awo amu CAF.
Masewero-wa akachitikira ku Bulawayo mdziko-lo.
Kotoko 4 Kano pillar 0
Previouse matchs
Timu ya Platinum ya ku Zimbabwe ili mdziko muno patsogolo pa masewero awo Lamulungu ndi Nyasa Big Bullets.
Platinum ili ku Lilongwe ndipo ikuyembekezeka kufika ku Blantyre lero.
Big Bullets 2 - Platinum 0