Timu ya Silver Strikers Ladies yalengeza kuti yatenga katswiri wotchinga pagolo Evelyn Kamanga kuchokera ku CY Sisters ya mchigawo chakumpoto.
Kamanga watikitira mgwirizano wa zaka zitatu ndi akatswiri a NBM Women's Premiership omwenso akayimilire dziko lino mu mpikisano wa masewero opitira ku CAF Women's Champions League pa mayiko amu COSAFA.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores