Mphunzitsi wamdziko la Spain, Indoni Iraola wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timu ya Liverpool kuti ayitsogolere timuyi.
Iye walowa mmalo mwa Anne Slot yemwe anachotsedwa kutsatira kuvutika kwa timuyi mu Chaka cha mpira cha 2025 mpaka 2026.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores