Koma malonjezo wa admin akugwila ntchito? Nanga a sabata yothera August 2 mwalandira photo zanu?
Ya ndizokwiyitsa kwambili m'paka pano sitinalandilebe a sabata yothela Augsburg 2.
Zoona zenizeni, mwina a president wathu a Ezala sakutithandiza maka akamakambilana ndi admin. Zoona zake mwina photo sadzaperekaso akukana kunena chilungamo
Yes, pafunika tikhale anthu oganiza sikuti azachita kutiuza kuti basi sitizalipilaso koma tokha tiwone mwomwe zukhalira ndipo akumalonjeza koma osakwanilitsa. Whay?
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores