Moni admin wathu. Tsopano zinthu zikutidabwitsa malingana ndimomwe zikuyendela maka kapelekedwe kamphoto yandalama yomwe olosera bwino kuposa anzawo amalandira pomwe asabata yothera 28 June sanalandirebe padutsa sabata ziwili tsopano zomwe sizikusangalatsa tose okonda kulosera masewela pa owinna.com. Kodi kapena pali vuto lina lomwe lupangitsa zimenezi? Ngati sichoncho tikupempha muzipereka photozi ngati kale chifukwa izi zikupereka chikaiko chokhulupilira page ya owinna.com
M'paka sabata kumatha?
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores