Salima, Malawi
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
MAFCO has commenced 2020 football preparations ahead of the country's formidable league kickoff.
Media Officer for the Club, Vanclayton Damaster, confirmed the development to Owinna.
Bungwe loyendetsa masewero m'chigawo cha pakati la CRFA laimitsa masewero a timu ya Luanar mu ligi ya Chipiku kutsatira mpungwepungwe womwe unalipo pa masewero awo ndi MAFCO.
Guyz Team Ya Silver Strikers Mukuiwona Bwanji Mu Season Ino....?
Wosewera mmbali mu timu ya Blue Eagles, Vitumbuko Kumwenda, sapezeka pa masewero a timuyi ndi MAFCO mu FISD kaamba kovulala.
Mphunzitsi wa timuyi, Deklerk Msakakuona, watsimikiza za nkhaniyi.
Mtsogoleri wa osewera wa timu ya MAFCO, Paul Ndlovu, wati ali ndi chikhulupiliro kuti abwelera mu ligi ya TNM potengera momwe akuchitira.
MAFCO on Sunday used bips in their game against Green Rangers.
It is reported that the two teams jeserys were similar.
PRELIMINARY ROUND 2/2:
MAFCO vs Mzuni Karonga United vs Ekwendeni Hammers Masters Security vs Red Lions Silver Strikers Reserve vs Mlatho Mponela.
ROUND of 16 1/2:
TN Stars vs Sable/Moyale Barracks MAFCO/Mzuni vs Blue Eagles Dwangwa United/Ntopwa vs Kamuzu Barracks Silver Strikers vs Silver Strikers Reserve/Mlatho Mponela.
MAFCO coach, Stereo Gondwe, is upbeat of returning to the country's elite league following a 5 point gap with the 2nd team in Chipiku Premier Division.
Gondwe said this in an interview with Owinna.
Matimu a zigawo omwe atenge nawo mbali ndi Red Lions, Sable Farming, Hangover, Airborne Rangers, Silver Strikers Reserves, MAFCO, Baka City ndi Ekwendeni Hammers.
Mphunzitsi wa MAFCO, Stereo Gondwe, wati pomwe akuyamba ndime yachiwiri ya Chipiku aonetsetsa kuti apambane masewero ochuluka.Gondwe wati iyi ndi njira yokhayo ipangitse timuyi kubwelera mu ligi ya TNM.
Note that Luanar games over the weekend have been postponed.
Luanar was supposed to play with Mafco and Lake Valley.
Osewera a MAFCO ajambula kanema yemwe akuyankha zomwe Khuda Muyaba ananena kuti ku Malawi kulibe mpira.
Mu kanema-yu osewera-wa atchula osewera akale omwe anali ku Silver Strikers.
Mafco head coach, Stereo Gondwe, says his team will return into TNM Super League with no doubts after collecting 6 points from the first 2 matches they have played so far.
Timu ya Mafco yati zokonzekera zake zikuyenda bwino pomwe ati akhulupilira kuti akhala ndi season yopambana mu ligi ya Chipiku.
MAFCO has started 2019 preparations on a high note with the intention of being crowned champions of Chipiku Premier League.
Officials of the club have stated that no player will leave the team.
Matimu a Airborne Rangers, Cobbe Barracks, MAFCO, Support Battalion, Changalume Barracks, Chilumba barracks, MDF Marine ndi Zomba Airwing akuyembekezeka kusewera nawo mu mpikisano wa Inter Unit Sports.
Wawa
Red Lions has been relegated from the TNM Super League after suffering a 3 nil defeat at Balaka Stadium against Nyasa Big Bullets. Other teams that have been relegated are MAFCO FC and Nchalo United
ROUND OF 16 DRAW (1/2): Kamuzu Barracks vs Marka Express, Silver Strikers vs Civo Sporting, Dwangwa Town Hammers vs BE FORWARD Wanderers, MAFCO vs Chitipa United.
ROUND OF 16: Hangover/Chitipa v Moyale Mchengautuwa/M Ivory v Tigers Ekwendeni H/Steffords v B Eagles BFW v Dwangwa Changalume/Ngolowindo v NBB/Mitundu Red L v TN Stars Masters v Cobbe/Airborne MAFCO v Silver S
Karonga Utd v BF Wanderers Nyasa Big Bullets v Mitundu Nyasa Bullets Reserve v Moyale Azam Tigers v KB MAFCO v Namingomba TN Stars v Civil Sporting MDF Marine v Blue Eagles Lilongwe Veterans v Silver Strikers