Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu ya Mlatho Mponela yalembera bungwe la CRFA kuti aisungire malo ake mu ligi ya Chipiku pomwe yati izatenga nawo mbali mu mpikisano-wu chaka chamawa.
Timu ya Mlatho Mponela yati itenga nawo mbali mu mpikisano wa Chipiku wa chaka chino.
Mmodzi wa akuluakulu a timuyi, Chiyamiko Litta, wati achita chotheka kuti abwelere mu ligi ya TNM.
Madeira from team manager at Nomads to Mlatho CEO - Malawi Nyasa Times Maverick sportsman Steve Madeira the former Br Forward Wanderers team manager has been hired by TNM Super League debutantes... www.nyasatimes.com