Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Victor Limbani wachoka ku timu ya Silver Strikers kutsatira kutha kwa kontrakiti yake pa 31 August, 2020.
Mkulu woyendetsa zintchito za timuyi, Thoko Chimbali, wati wosewerayu anali wapamwamba.
Timu ya Silver Strikers yaonjezera m'ndandanda wa osewera omwe yachotsa kufika pa 20.
Izi zikutsaira kuchotsedwa kwa Victor Limbani komanso Hygiene Mwendepeka.
First Match Dwangwa United 0 - 3 Silver Strikers (Zikani Kasambala, Victor Limbani [2])
Second Match Dwangwa United 2 - 0 Silver Strikers ?
Timu ya Silver Strikers inapambana masewero ake oyamba ndi Dwangwa United ndi zigoli zitatu kwa dhu. Pa masewero-wa Zikani Kasambala anamwetsa chigoli chimodzi, Victor Limbani anagoletsa zigoli ziwiri.
FT: Silver Strikers 12 - 0 Chulu (3x Victor Limbani, 3x Tizgowere Kumwenda, 3x Binwell Katinji, 2x Levison Maganizo, Matthews Sibale)
FT: Civo United 1 - 2 Silver Strikers (Nelson Kangunje - Victor Limbani, Green Harawa)
FT: Civo United 1 - 2 Silver Strikers (? - Victor Limbani, Green Harawa)
H2: Civo United 0 - 2 Silver Strikers (Victor Limbani, Green Harawa)
H1: Civo United 0 - 1 Silver Strikers (Victor Limbani)
FT: BE FORWARD Wanderers 0 - 2 Silver Strikers (57' Green Harawa, Victor Limbani)
80' BE FORWARD Wanderers 0-2 Silver Strikers (57' Green Harawa, Victor Limbani)
FT: Silver Strikers 3 - 1 Moyale Barracks (Peter Wadabwa, Victor Limbani, Green Harawa - Ntopijo Njerwa) (on Saturday, 16th May 2015)
FT: Big Bullets 2 - 0 Zomba United (Victor Limbani, Henry Kabichi)
FT: Silver Strikers 1 - 2 Big Bullets (Ndaziona Chatsalira - Victor Limbani, Pilirani Zonda)
FT: Red Lions 0 - 2 Big Bullets (Victor Limbani, Jimmy Zakazaka)
FT: Big Bullets 1 - 0 Kamuzu Barracks (Victor Limbani)
FT: Blantyre United 1 - 1 Mponela United (Victor Limbani - Harold Mpima)
FT: Blantyre United 3 - 2 Red Lions (Victor Limbani, Sparrow Msowoya, Jimmy Chikulekule - Kelvin Katema)
FT: Blantyre United 3 - 0 Moyale Barracks (2x Muhammad Sulumba, Victor Limbani)