Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
CHAZIYA AZIBWERERA KUMUDZI
Katswiri watimu ya Mighty Mukuru Wanderers, Lawrence Chaziya, akuyembekezeka kubwerera kumudzi pomwe tsopano timu ya TP Mazembe yatsimikiza kuti sasayinidwanso.
Malingana ndi mkhalapakati wa osewerayu, Felix Ngamanya Sapao, watsimikiza kuti katswiriyu sapatsidwa mgwirizano ndi timuyi kamba ka zifukwa zomwe sanazinene.
Iye koma watsimikiza kuti osewera a FCB Nyasa Big Bullets, Patrick Mwaungulu ndi Lanjesi Nkhoma, akhale akusaina migwirizano yawo ndi timuyi.
Iye koma watinso ngakhale osewerawa amayenera kusainiratu migwirizano, timuyi inasankhanso kuti iwaunikire mphamvu zawonso.
Izinso ndi malingana mmene olemba nkhani wa mdziko lino, Twaha Chimuka analembera lamulungu kuti Chaziya abwerera kumudzi kuno.
CHAZIYA CONFIRMS HE IS COMING BACK
Mighty Mukuru Wanderers captain, Lawrence Chaziya, has confirmed that he will be returning to Malawi after his deal flopped at TP Mazembe.
Chaziya wrote this through his Facebook page after Twaha Chimuka revealed it on Sunday that the player will return to Malawi due to age cheating claims.
"Itβs true am coming home π²πΌ. Thank you so much God β€οΈππ." Wrote Chaziya.
Meanwhile, his agent, Felix Ngamanya Sapao, also confirmed this morning that the team will continue to sign Patrick Mwaungulu and Lanjesi Nkhoma only.
He will return at the Nomads amidst the period when the team was looking for his replacement following woes in the team's defense since he left for DRC.
"CHOMWE TIKUNGOFUNAPO NDI CHIPAMBANO BASI" - CHAZIYA
Mtsogoleri wa osewera kutimu ya Mighty Mukuru Wanderers, Lawrence Chaziya, walimbitsa mtima otsatira a timuyi kuti iwo apeza chipambano pomwe akukumana ndi FCB Nyasa Big Bullets loweruka mu TNM Supa ligi.
Iye amayankhula lachisanu patsogolo pa masewerowa pa bwalo la Kamuzu ndipo wati osewera onse alibwino ndipo molalo ili pamwamba pomwe akufuna kukagonjetsa Bullets.
"Takonzekera bwino kwambiri masewerowa ndipo mu camp mwathu molalo ndi yapamwamba pomwe tikukakumana ndi anzathuwa, chabwino Bullets ndi timu yabwino ifenso ndi timu yabwino koma tikungofunapo 3 points basi." Anafotokoza Chaziya.
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers ikuyang'ana chipambano chawo choyamba pamwamba pa Bullets pomwe anayigonjetsa komaliza mu 2021.
Manoma ali pa nambala yachitatu mu ligi pomwe yapezako mapointsi asanu ndi atatu pa masewero anayi.
CHAZIYA OUT FOR THREE WEEKS
Mighty Mukuru Wanderers captain, Lawrence Chaziya, will not be available for three weeks after being ruled out due to injury.
The Nomads has confirmed the news on Tuesday after tests by the doctors and the defender could be doubt again for the Blantyre Derby on 4 May 2024.
He was stretched out on 42nd minute of the Nomads 3-0 win over FOMO FC last Sunday and Peter Cholopi replaced him.
The Nomads will now rely on Peter Cholopi, Chimwemwe Nkhoma, Ahamad Kungunde and Emmanuel Nyirenda as Center backs at the team.
Chaziyaβs agent shuns local clubs - The Nation Online Β Flames centre-back Lawrence Chaziyaβs managers Royal Soccer Scout have ruled out the possibility of the player signing for a TNM Super League... mwnation.com