Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Mphekesera zomwe zumveka masamba a mchezo kuti mbali ina la bwalo la Bingu lagwa ndi zabodza.
Owinna itayendera bwaloli lapeza kuti zonse zili n'chimake pa bwaloli.
Anthu ena okonda masewero mdziko muno ayankhulapo za chibaluwa chomwe chikuyenda masamba a mchezo choonetsa zomwe a Nyamilandu achita.
Anthu-wa ayamikira mtsogoleri-yu koma ati asapikisane nawo.
Wanderers yatsutsa malipoti oti yasiya osewera ena monga mmene anthu akunenera pa masamba a mchezo a intaneti.
Anthu ena akufalitsa kuti timuyi yasiya Alfred Manyozo komanso Harry Nyirenda kumpoto.